1 Samuel 20:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mnyamatayo sadadziŵe kanthu ai, Yonatani yekha ndi Davide ndiwo amene ankadziŵa zimene zinkachitika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mnyamatayo sanadziwe kanthu; Davide ndi Yonatani okha anadziwa za mlanduwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Mnyamatayo sanadziwe chimene chimachitika koma Yonatani ndi Davide ndiwo ankadziwa).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mnyamatayo sanadziwa kanthu; Davide ndi Jonatani okha anadziwa za mranduwoo.