1 Samuel 20:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Yonatani adapereka zida zake kwa mnyamata wake uja, namuuza kuti, “Pita, kazitule ku mzinda.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yonatani anapatsa mnyamata wake zida zake, nanena naye, Muka, tenga izi kunka nazo kumudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Yonatani anapereka zida zake za nkhondo kwa mnyamatayo ndipo anati, “Pita, nyamula ubwerere nazo ku mzinda.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Jonatani anapatsa mnyamata wace zida zace, nanena naye, Muka, tenga izi kunka nazo kumudzi.