1 Samuel 20:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akati, ‘Chabwino’, zinthu zidzandiyendera bwino, ine kapolo wako. Koma akakhala wokwiyabe, udziŵe kuti watsimikiza mtima kuti andichita choipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono akati, Chabwino; kapolo wako adzakhala ndi mtendere; koma akapsa mtima, uzindikirepo kuti anatsimikiza mtima kundichitira choipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akanena kuti, ‘Wachita bwino,’ ndiye kuti zinthu zindiyendera bwino ine mtumiki wako. Koma ngati akapsa mtima, ndiye udziwe kuti iwo atsimikiza zondichita zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono akati, Cabwino; kapolo wako adzakhala ndi mtendere; koma akapsa mtima, uzindikirepo kuti anatsimikiza mtima kundicitira coipa.