1 Samuel 21:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lomwelo Davide adanyamuka kuthaŵa Saulo, ndipo adapita kwa Akisi mfumu ya ku Gati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide ananyamuka, nathawa tsiku lomwelo chifukwa cha kuopa Saulo, namuka kwa Akisi mfumu ya ku Gati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lomwelo Davide ananyamuka kuthawa Sauli ndipo anapita kwa Akisi, mfumu wa ku Gati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide ananyamuka, nathawa tsiku lomwelo cifukwa ca kuopa Sauli, namuka kwa Akisi mfumu ya ku Gati.