1 Samuel 21:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau ameneŵa Davide adamloŵa mu mtima kwambiri, ndipo adayamba kuwopa Akisi mfumu ya ku Gati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anasunga mau awa mumtima mwake, naopa kwambiri Akisi mfumu ya Gati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawu amenewa anamulowa kwambiri Davide mu mtima ndipo anayamba kuopa kwambiri Akisi mfumu ya ku Gati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anasunga mau awa mumtima mwace, naopa kwambiri Akisi mfumu ya Gati.