1 Samuel 21:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Akisi adauza nduna zake kuti, “Mukuwona kuti munthuyu ngwamisala. Chifukwa chiyani tsono mwabwera naye kwa ine?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono Akisi ananena ndi anyamata ake, Taonani, mupenya kuti munthuyo ngwa misala; mwabwera naye kwa ine chifukwa ninji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akisi anawuza nduna zake kuti, “Mukumuona munthu uyu kuti ndi wamisala! Nʼchifukwa chiyani mukubwera naye kwa ine?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono Akisi ananena ndi anyamata ace, Taonani, mupenya kuti munthuyo ngwa misala; mwabwera naye kwa ine cifukwa ninji?