1 Samuel 21:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi muli ndi chakudya? Mundipatseko mitanda isanu yabuledi kapena chakudya chilichonse chimene muli nacho pano.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake tsono muli ndi chiyani? Mundipatse m'dzanja langa mikate isanu, kapena chilichonse muli nacho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi muli ndi chakudya? Patseniko malofu a buledi asanu, kapena chilichonse muli nacho.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace tsono muli ndi ciani? mundipatse m'dzanja langa mikate isanu, kapena ciri conse muli naco.