1 Samuel 22:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Saulo adati, “Imva tsono, iwe mwana wa Ahitubi.” Iye adayankha kuti, “Inde, mbuyanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo anati, Imva tsopano iwe mwana wa Ahitubi. Nayankha iye, Ndine, mbuye wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli anati, “Tsono tamvera, mwana wa Ahitubi.” Iye anayankha kuti, “Inde mbuye wanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli anati, Imva tsopano iwe mwana wa Ahitubu. Nayankha iye, Ndine, mbuye wanga.