1 Samuel 22:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mmodzi mwa ana aamuna a Ahimeleki, mwana wa Ahitubi, dzina lake Abiyatara, adapulumuka, nathaŵa kutsatira Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mmodzi wa ana a Ahimeleki, mwana wa Ahitubi, dzina lake ndiye Abiyatara, anapulumuka, nathawira kwa Davide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Abiatara mwana wa Ahimeleki mwana wa Ahitubi anapulumuka ndi kuthawira kwa Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mmodzi wa ana a Ahimeleki, mwana wa Ahitubu, dzina lace ndiye Abyatara, anapulumuka, nathawira kwa Davide.