1 Samuel 22:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adaŵasiya kumeneko makolo akewo kwa mfumu ya ku Mowabuko, ndipo iwo adakhala komweko nthaŵi yonse imene Davide ankabisala kuphanga kuja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawatenga kunka nao pamaso pa mfumu ya Mowabu; ndipo iwo anakhala naye nthawi yonse Davide anali ku lingalo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho iye anawasiya kwa mfumu ya Mowabu ndipo anakhala naye nthawi yonse imene Davide ankabisala ku phanga kuja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawatenga kumka nao pamaso pa mfumu ya Moabu; ndipo iwo anakhala naye nthawi yonse Davide anali ku lingalo.