1 Samuel 22:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Doegi Mwedomu, amene adaaimirira pafupi ndi nduna za Saulo, adanena kuti, “Ine ndidamuwona mwana wa Yese akupita ku Nobu kwa Ahimeleki, mwana wa Ahitubi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Doegi wa ku Edomu, anaimirira ndi anyamata a Saulo, nayankha, nati, Ine ndinamuona mwana wa Yeseyo alikufika ku Nobu, kwa Ahimeleki mwana wa Ahitubi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Doegi Mwedomu anayima pafupi ndi nduna za Sauli nati, “Ine ndinaona mwana wa Yese atabwera kwa Ahimeleki mwana wa Ahitubi ku Nobi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Doegi wa ku Edomu, anaimirira ndi anyamata a Sauli, nayankha, nati, Ine ndinamuona mwana wa Jeseyo alikufika ku Nobi, kwa Ahimeleki mwana wa Ahitubu.