1 Samuel 23:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina Davide adamva kuti Afilisti akuthira nkhondo mzinda wa Keila, ndipo akufunkha zokolola za m'nkhokwe zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono anauza Davide, kuti, Onani Afilisti alikuponyana ndi Keila, nafunkha za m'madwale.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide atawuzidwa kuti “Onani, Afilisti akuthira nkhondo mzinda wa Keila ndi kulanda zokolola zawo za mʼnkhokwe,”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono anauza Davide, kuti, Onani Afilisti alikuponyana ndi Keila, nafunkha za m'madwale.