1 Samuel 23:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide ankabisala m'mapanga m'dziko lamapiri ku chipululu cha Zifi. Monsemo Saulo ankamufunafuna, koma Mulungu sadalole kuti agwidwe ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anakhala m'chipululu m'ngaka, nakhala m'dziko la mapiri m'chipululu cha Zifi. Ndipo Saulo anamfunafuna masiku onse, koma Mulungu sadampereka m'dzanja lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide ankakhala mʼmapanga mʼdziko lamapiri ku chipululu cha Zifi. Sauli ankamufufuza tsiku ndi tsiku, koma Mulungu sanapereke Davide mʼmanja mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anakhala m'cipululu m'ngaka, nakhala m'dziko la mapiri m'cipululu ca Zifi. Ndipo Sauli anamfunafuna masiku onse, koma Mulungu sadampereka m'dzanja lace.