1 Samuel 23:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yonatani, mwana wa Saulo, adanyamuka napita kwa Davide ku Horesi, ndipo adamlimbitsa mtima pomuuza kuti Mulungu adzamteteza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yonatani mwana wa Saulo ananyamuka, napita kwa Davide kunkhalangoko, namlimbitsa dzanja lake mwa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yonatani mwana wa Sauli anapita kwa Davide ku Horesi ndipo anamulimbitsa mtima pomuwuza kuti Yehova ali naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Jonatani mwana wa Sauli ananyamuka, napita kwa Davide kunkhalangoko, namlimbitsa dzanja lace mwa Mulungu.