1 Samuel 23:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yonatani adauza Davide kuti, “Usaope, abambo anga sadzakupha. Udzakhala mfumu ya Aisraele, ndipo ine ndidzakhala wachiŵiri kwa iwe. Abambo angawo akudziŵanso zimenezi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye ananena naye, Usaopa; chifukwa dzanja la Saulo atate wanga silidzakupeza; iwe udzakhala mfumu ya Israele, ndipo ine ndidzakhala wotsatana nawe, ichinso Saulo atate wanga achidziwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anamuwuza kuti, “Usaope, abambo anga sadzakupha. Iwe udzakhala mfumu ya Israeli ndipo ine ndidzakhala wachiwiri wako. Ngakhale abambo anga Sauli akudziwa zimenezi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye ananena naye, Usaopa; cifukwa dzanja la Sauli atate wanga silidzakupeza; iwe udzakhala mfumu ya Israyeli, ndipo ine ndidzakhala wotsatana nawe, icinso Sauli atate wanga acidziwa.