1 Samuel 23:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Davide adafunsa Chauta kuti, “Kodi ndikamenyane nawo nkhondo Afilistiwo?” Chauta adamuuza kuti, “Pita, kamenyane nawo, kuti upulumutse mzinda wa Keila.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Davide anafunsira kwa Yehova, nati, Ndimuke kodi kukakantha Afilisti aja? Ndipo Yehova anati kwa Davide, Muka, nukanthe Afilisti, ndi kupulumutsa Keila.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anafunsa Yehova kuti, “Kodi ndipite ndikamenyane nawo Afilistiwa?” Yehova anamuyankha kuti, “Pita, kamenyane nawo Afilisti ndi kupulumutsa mzinda wa Keila.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Davide anafunsira kwa Yehova, nati, Ndimuke kodi kukakantha Afilisti aja? Ndipo Yehova anati kwa Davide, Muka, nukanthe Afilisti, ndi kupulumutsa Keila.