1 Samuel 23:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono inu amfumu, ife tadziŵa kuti mukumfunafuna kwambiri, choncho bwerani ndithu. Ifeyo tidzampereka kwa inu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake mfumu, tsikani, monga umo mukhumbire m'mtima mwanu kutsika; ndipo kudzakhala kwathu kumpereka iye m'dzanja la mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano inu, mubwere nthawi iliyonse imene mukufuna, ndipo ife tidzamupereka kwa mfumu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace mfumu, tsikani, monga umo mukhumbire m'mtima mwanu kutsika; ndipo kudzakhala kwathu kumpereka iye m'dzanja la mfumu.