1 Samuel 23:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Saulo adati, “Chauta akudalitseni, pakuti mwandikomera mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Saulo nati, Mudalitsike inu kwa Yehova; chifukwa munandichitira ine chifundo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli anayankha kuti, “Yehova akudalitseni pakuti mwandichitira chifundo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sauli nati, Mudalitsike inu kwa Yehova; cifukwa munandicitira ine cifundo.