1 Samuel 23:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pitani mukaonetsetse. Mukafufuze kumene kuli mbuto yake, ndi kupeza munthu amene wamuwona chamaso kumeneko. Ndikumva kuti ngwochenjera mwaukapsala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukanitu kuti mukadziwitse ndithu, ndi kudziwa ndi kuona mbuto m'mene akhalitsa, ndi amene adamuona m'menemo; chifukwa anandiuza kuti iye achita mochenjera ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pitani mukatsimikizire. Mukaone kumene amakhala ndiponso mupeze munthu amene wamuona. Anthu amandiwuza kuti ndi wochenjera kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukanitu kuti mukadziwitse ndithu, ndi kudziwa ndi kuona mbuto m'mene akhalitsa, ndi amene adamuona m'menemo; cifukwa anandiuza kuti iye acita mocenjera ndithu.