1 Samuel 23:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi yomweyo padafika wamthenga amene adauza Saulo kuti, “Mufulumire kubwera, pakuti Afilisti akulithira nkhondo dzikoli.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mthenga unafika kwa Saulo ndi kuti, Mufulumire kubwerera; popeza nkhondo yovumbulukira ya Afilisti yalowa m'dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi yomweyo munthu wina wamthenga anabwera kudzamuwuza Sauli kuti, “Bwerani msanga! Afilisti akuthira nkhondo dzikoli.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mthenga unafika kwa Sauli ndi kuti, Mufulumire kubwerera; popeza nkhondo yobvumbulukira ya Afilisti yalowa m'dziko.