1 Samuel 23:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Saulo adasonkhanitsa ankhondo ake, naŵatuma ku Keila kuti akamzinge Davide pamodzi ndi anthu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo anamemeza anthu onse kunkhondo, kuti atsikire ku Keila, kumangira misasa Davide ndi anthu ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Sauli anasonkhanitsa ankhondo ake nawatuma ku Keila kuti akamuzungulire Davide ndi anthu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli anamemeza anthu onse kunkhondo, kuti atsikire ku Keila, kumangira misasa Davide ndi anthu ace.