1 Samuel 23:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Davide adaadziŵa kuti Saulo akufuna kumchita chiwembu. Choncho adauza wansembe Abiyatara kuti abwere ndi efodi ija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anadziwa kuti Saulo analikulingalira zomchitira zoipa; nati kwa Abiyatara wansembe, Bwera kuno ndi efodi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide atadziwa kuti Sauli akufuna kumuchita chiwembu, anawuza Abiatara wansembe uja kuti, “Bwera nayo efodiyo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anadziwa kuti Sauli analikulingalira zomcitira zoipa; nati kwa Abyatara wansembe, Bwera kuno ndi efodi.