1 Samuel 24:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lero waonetsa ubwino wako pakuti sudandiphe, Chauta atandipereka kwa iwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo unatsimikiza lero lino kuti wandichitira zabwino; chifukwa sunandipha pamene Yehova anandipereka m'dzanja lako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iweyo lero lino wandifotokozera zabwino zimene wandichitira. Yehova anandipereka mʼdzanja lako koma iwe sunandiphe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo unatsimikiza lero lino kuti wandicitira zabwino cifukwa sunandipha pamene Yehova anandipereka m'dzanja lako.