1 Samuel 25:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nabala adayankha anyamata a Davide aja poŵafunsa kuti, “Kodi Davide mwana wa Yese ndani? Ha! Masiku ano pali anthu antchito ambiri amene akuthaŵa kwa ambuyao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Nabala anayankha anyamata a Davide nati, Davide ndani? Ndi mwana wa Yese ndani? Makono ano pali anyamata ambiri akungotaya ambuye ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nabala anayankha anyamata a Davide kuti, “Kodi Davide ndi ndani? Mwana wa Yese ndi ndani? Masiku ano pali antchito ambiri amene akuthawa kwa mabwana awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Nabala anayankha anyamata a Davide nati, Davide ndani? ndi mwana walese ndani? Makono ano pali anyamata ambiri akungotaya ambuye ao.