1 Samuel 25:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndingatenge chakudya changa, madzi anga, nyama yanga imene ndaphera anyamata anga ometa nkhosa, kuti ndipatse anthu omwe sindikudziŵa kumene akuchokera?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi ndidzatenga mkate wanga, ndi madzi anga, ndi nyama imene ndinaphera osenga nkhosa anga, ndi kuzipatsa anthu amene sindidziwa kumene afumira?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nditengerenji buledi, madzi ndi nyama zimene ndaphera anthu anga ometa nkhosa ndi kuzipereka kwa anthu amene sindikudziwa kumene achokera?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi ndidzatenga mkate wanga, ndi madzi anga, ndi nyama imene ndinaphera osenga nkhosa anga, ndi kuzipatsa anthu amene sindidziwa kumene afumira?