1 Samuel 25:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho anyamata a Davide adapotoloka, nabwerera kukauza Davide zonsezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwecho anyamata a Davide anatembenukira ku njira yao, nabwerera, nadza namuuza monga mwa mau onse awa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anyamata a Davide aja anatembenuka nabwerera. Atafika anafotokozera Davide mawu onse a Nabala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweco anyamata a Davide anatembenukira ku njira yao, nabwerera, nadza namuuza monga mwa mau onse awa.