1 Samuel 25:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe anthu amenewo adatichitira zabwino osati zoipa, poti sitidasoŵe kanthu nthaŵi zonse pamene tinali ndi iwowo ku busa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anthu aja anatichitira zabwino ndithu, sanatichititse manyazi, ndi panalibe kanthu kadatisowa, nthawi zonse tinali kuyenderana nao kubusa kuja;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komatu anthuwa anatichitira zabwino kwambiri. Sanatizunze, ndipo nthawi yonse imene tinali nawo ku busa sitinasowe kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anthu aja anaticitira zabwino ndithu, sanaticititsa manyazi, ndi panalibe kanthu kadatisowa, nthawi zonse tinali kuyenderana nao kubusa kuja;