1 Samuel 25:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankatichinjiriza ngati linga usana ndi usiku, nthaŵi zonse pamene tinali ndi iwowo poŵeta nkhosa ku Rama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iwo anatikhalira ngati linga usana ndi usiku, nthawi yonse tinali nao ndi kusunga nkhosazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ankatitchinjiriza ngati mpanda usiku ndi usana nthawi yonse tinkaweta nkhosa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iwo anatikhalira ngati linga usana ndi usiku, nthawi yonse tinali nao ndi kusunga nkhosazo.