1 Samuel 25:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adauza anyamata ake antchito kuti, “Batsogolani, ine ndikudza pambuyo panu.” Koma sadauze Nabala mwamuna wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati kwa anyamata ake, Nditsogolereni; onani ndidza m'mbuyo mwanu. Koma sanauze mwamuna wake Nabala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anawuza antchito ake kuti, “Tsogolani, ine ndikutsatirani.” Koma sanawuze mwamuna wake Nabala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati kwa anyamataace, Nditsogolereni; onani ndidza m'mbuvo mwanu. Koma sanauza mwamuna wace Nabala.