1 Samuel 25:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu andilange ndithu ngati m'maŵa ndikhale nditasiyapo ngakhale munthu wamwamuna mmodzi mwa anthu onse amene ali nawo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu alange adani a Davide, ndi kuonjezerapo, ngati ndisiyapo kufikira kuunika kwa m'mawa, kanthu konse ka iye, kangakhale kamwana kamphongo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu andilange kwambiri ngati pofika mmawa nditakhale nditasiyako ngakhale munthu mmodzi mwa onse amene ali nawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu alange adani a Davide, ndi kuonjezerapo, ngati ndisiyapo kufikira kuunika kwa m'mawa, kanthu konse ka iye, kangakhale kamwana kamphongo.