1 Samuel 25:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pepani, nazi mphatsozi zimene mdzakazi wanune ndabwera nazo kwa inu mbuyanga, kuti zipatsidwe kwa anthu muli nawoŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mphatso iyi mdzakazi wanu ndatengera mbuye wanga, ipatsidwe kwa anyamata akutsata mbuye wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho, nazi mphatso zimene mdzakazi wanu ndabwera nazo kwa mbuye wanga kuti zipatsidwe kwa anyamata amene muli nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mphatso iyi mdzakazi wanu ndatengera mbuye wanga, ipatsidwe kwa anyamata akutsata mbuye wanga.