1 Samuel 25:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mbuyanga, Chauta adzakuchitirani zabwino zonse zimene adakulonjezani, ndipo adzakuikani kuti mukhale mfumu yolamulira Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzali, pamene Yehova anachitira mbuye wanga monga mwa zabwino zonse adalankhula za inu, ndipo adadzaika inu mukhale kalonga wa Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova adzakuchitirani mbuye wanga zabwino zonse zimene anakulonjezani. Adzakuyikani kukhala wolamulira Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzali, pamene Yehova anacitira mbuye wanga monga mwa zabwino zonse adalankhula za inu, ndipo adadzaika inu mukhale kalonga wa Israyeli;