1 Samuel 25:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu akudalitseni chifukwa cha nzeru zimene mwaonetsa lero pondiletsa kuti ndisakhetse magazi ndi kulipsira ndi manja anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo, kudalitsike kuchenjera kwako, nudalitsike iwe, pakuti unandiletsa kusakhetsa mwazi, ndi kusabwezera chilango ndi dzanja la ine ndekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akudalitseni chifukwa cha nzeru zanu pondiletsa lero kuti ndisakhetse magazi ndi kubwezera adani anga ndi manja anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo, kudalitsike kucenjera kwako, nudalitsike iwe, pakuti unandiletsa kusakhetsa mwazi, ndi kusabwezera cilango ndi dzanja la ine ndekha.