1 Samuel 25:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide anali atamva kuchipululu kuja kuti Nabala akumeta nkhosa zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anamva kuchipululu kuti Nabala alinkusenga nkhosa zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anamva akanali ku chipululu kuti Nabala akumeta nkhosa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anamva kucipululu kuti Nabala alinkusenga nkhosa zace.