1 Samuel 25:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anyamata a Davide atafika kwa Abigaile ku Karimele, adamuuza kuti “Mfumu Davide watituma kuti tikutengeni, mukakhale mkazi wake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anyamata a Davide pakufika kwa Abigaile ku Karimele, analankhula naye, nati, Davide anatitumiza kwa inu, kukutengani, mukhale mkazi wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anyamata a Davide atafika ku Karimeli anawuza Abigayeli kuti, “Davide watituma kwa iwe kuti tikutenge ukhale mkazi wake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anyamata a Davide pakufika kwa Abigayeli ku Karimeli, analankhula naye, nati, Davide anatitumiza kwa inu, kukutengani, mukhale mkazi wace.