1 Samuel 25:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkaziyo adagwada nagunditsa nkhope yake pansi, nati, “Ine mdzakazi wa mbuyanga Davide, ndili wokonzeka ngakhale kusambitsa mapazi a anyamata ake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye ananyamuka, nawerama nkhope yake pansi, nati, Onani, mdzakazi wanu ali kapolo wakusambitsa mapazi a anyamata a mbuye wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abigayeli anagwada nagunditsa nkhope yake pansi ndipo anati, “Ine mdzakazi wa mbuye wanga ndakonzeka kutumikira ngakhale kusambitsa mapazi a anyamata ake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye ananyamuka, nawerama nkhope yace pansi, nati, Onani, mdzakazi wanu ali kapolo wakusambitsa mapazi a anyamata a mbuye wanga.