1 Samuel 25:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Saulo anali atakwatitsa mwana wake Mikala, mkazi wa Davide, kwa Paliti mwana wa Laisi wa ku Galimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Saulo anapatsa Mikala, mwana wake, mkazi wa Davide, kwa Paliti mwana wa Laisi, wa ku Galimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Sauli anali atakwatitsa Mikala, mkazi wa Davide kwa Paliti mwana wa Laisi wa ku Galimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Sauli anapatsa Mikala, mwana wace, mkazi wa Davide, kwa Paliti mwana wa Loisi, wa ku Galimu.