1 Samuel 25:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adatuma anyamata khumi kuti, “Pitani ku phiri la Karimele kwa Nabala, mukandiperekere moni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Davide natuma anyamata khumi, nanena kwa anyamatawo, Mukwere ku Karimele, mumuke kwa Nabala ndi kundiperekera moni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anatuma anyamata khumi nawawuza kuti, “Pitani kwa Nabala ku Karimeli ndipo mukamulonjere mʼdzina langa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Davide natuma anyamata khumi, nanena kwa anyamatawo, Mukwere ku Karimeli, mumuke kwa Nabala ndi kundilankhulira iye;