1 Samuel 25:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikumva kuti muli ndi anthu ometa nkhosa. Pamene abusa anu anali nafe kuno, sitidaŵachite choipa chilichonse, ndipo sadasoŵe kanthu pa nthaŵi yonse pamene adakhala ku Karimele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsono ndamva kuti muli nao osenga nkhosa; abusa anu amene anali ndi ife, sitinawachititsa manyazi, ndipo panalibe kanthu kao kadasowa, nthawi yonse anakhala iwo ku Karimele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Tsono ndamva kuti muli ndi anthu ometa nkhosa. Pamene abusa anu anali nafe kuno, sitinawachite china chilichonse choyipa, ndipo sanasowe kanthu pa nthawi yonse imene anali ku Karimeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsono ndamva kuti muli nao osenga nkhosa; abusa anu amene anali ndi ife, sitinawacititsa manyazi, ndipo panalibe kanthu kao kadasowa, nthawi yonse anakhala iwo ku Karimeli.