1 Samuel 25:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anyamata a Davide aja atafika, adafotokozera Nabala zonse zimene Davide adaaŵauza. Ndipo iwowo adayembekeza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakufika anyamata a Davide, analankhula ndi Nabala monga mau aja onse m'dzina la Davide, naleka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anyamata a Davide aja atafika, anamuwuza Nabala zonse zimene Davide anayankhula. Ndipo anadikira yankho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakufika anyamata a Davide, analankhula ndi Nabala monga mau aja onse m'dzina la Davide, naleka.