1 Samuel 26:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina anthu a ku Zifi adabwera kwa Saulo ku Gibea, namuuza kuti, “Davide akubisala ku phiri la Hakila limene lili kuvuma kwa Yesimoni.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Azifi anafika kwa Saulo ku Gibea, nati, Kodi Davide sali kubisala m'phiri la Hakila, kupenya kuchipululu!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a ku Zifi anapita kwa Sauli ku Gibeya nati, “Davide akubisala ku phiri la Hakila, limene limayangʼanana ndi Yesimoni.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Azifi anafika kwa Sauli ku Gibeya, nati, Kodi Davide sali kubisala m'phiri la Hagila, kupenya kucipululu!