1 Samuel 26:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adalamulira kuti, “Pali Chauta wamoyo, Chautayo ndiye adzamkanthe kapena pamene lidzafike tsiku lake lakumwalira, kapena pamene adzapite ku nkhondo nakaphedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Davide, Pali Yehova, Yehova adzamkantha iye; kapena tsiku la imfa yake lidzafika; kapena adzatsikira kunkhondo, nadzafako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anati, Pali Yehova wamoyo, Yehova mwini ndiye adzamukanthe, mwina tsiku lake lomwalira lidzafika, kapena adzapita ku nkhondo nakaphedwa komweko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Davide, Pali Yehova, Yehova adzamkantha iye; kapena tsiku la imfa yace lidzafika; kapena adzatsikira kunkhondo, nadzafako.