1 Samuel 26:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Saulo adazindikira liwu la Davide, ndipo adafunsa kuti, “Kodi liwu limeneli ndi lako, iwe mwana wanga Davide?” Davide adayankha kuti, “Inde, ndi liwu langadi, mbuyanga mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Saulo anazindikira mau ake a Davide, nati, Ndi mau ako awa, mwana wanga Davide? Nati Davide, Ndi mau anga mfumu, mbuye wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sauli anazindikira mawu a Davide ndipo anafunsa kuti, “Kodi amenewa ndi mawu ako Davide mwana wanga?” Davide anayankha, “Inde ndi anga, mbuye wanga mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sauli anazindikira mau ace a Davide, nati, Ndi mau ako awa, mwana wanga Davide? Nati Davide, Ndi mau anga mfumu, mbuye wanga.