1 Samuel 26:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye inu tsono musalole kuti ndifere kutali ndi Chauta, pakuti mfumu ya Aisraele yatuluka kudzandifunafuna ine nthata, monga momwe amachitira munthu wosaka nkhwali ku thengo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake tsono, mwazi wanga usagwe pansi kutali ndi Yehova; pakuti mfumu ya Israele yatuluka kudzafuna nsabwe, monga munthu wosaka nkhwali pamapiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano musalole kuti magazi anga akhetsedwe kutali ndi Yehova pakuti mfumu ya Israeli yatuluka kudzafunafuna ine nsabwe, monga mmene munthu asakira nkhwali ku mapiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace tsono, mwazi wanga usagwe pansi kutati ndi Yehova; pakuti mfumu ya Israyeli yaturuka kudzafuna nsabwe, monga munthu wosaka nkhwali pamapiri.