1 Samuel 26:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Davide adayankha kuti, “Suwu mkondo wanu, mfumu. Tumani mmodzi mwa ankhondowo adzatenge.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Davide nayankha, nati, Tapenyani mkondo wa mfumu! Abwere mnyamata wina kuutenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anayankha kuti, “Nawu mkondo wanu, mfumu. Tumani mmodzi wa anyamata anu abwere adzatenge.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Davide nayankha, nati, Tapenyani lmkondo wa mfumu Abwere mnyamata wina kuutenga.