1 Samuel 26:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide adatuma anthu oti akazonde, ndipo adapezadi kuti Saulo wafika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Davide anatumiza ozonda, nazindikira kuti Saulo anabwera ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iye anatumiza anthu okazonda ndipo anapeza kuti Sauli wafikadi ndithu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Davide anatumiza ozonda, nazindikira kuti Sauli anabwera ndithu,