1 Samuel 28:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumuyo idamuuza kuti, “Usaope. Kodi ukuwona chiyani?” Mkaziyo adati, “Ndikuwona mzimu ukutuluka pansi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumuyo inanena naye, Usaope, kodi ulikona chiyani? Mkaziyo nanena ndi Saulo, Ndilikuona milungu ilikukwera kutuluka m'kati mwa dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumuyo inamuwuza kuti, “Usaope. Kodi ukuona chiyani?” Mkaziyo anayankha kuti, “Ndikuona mzimu ukutuluka pansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumuvo inanena naye, Usaope, kodi ulikuona ciani? Mkaziyo nanena ndi Sauli, Ndirikuona milungu irikukwera kuturuka m'kati mwa dziko.