1 Samuel 28:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samuele adati, “Chifukwa chiyani ukufuna ine tsopano, chikhalirecho Chauta wakufulatira kale ndipo wasanduka mdani wako?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Samuele ananena naye, Ndipo undifunsiranji ine, popeza Yehova anakuchokera, nasandulika mdani wako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samueli anati, “Nʼchifukwa chiyani ukundifunsa ine, pakuti tsopano Yehova wakufulatira ndipo wasanduka mdani wako?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndip'o Samueli ananena naye, Ndipo undifunsiranji ine, popeza Yehova anakucokera, nasandulika mdani wako?