1 Samuel 28:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Saulo adakana nati, “Ine sindidya ai.” Koma nduna zake pamodzi ndi mkaziyo adamkakamiza, ndipo adaŵamvera. Choncho adadzuka pansi paja nakhala pa bedi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye anakana, nati, Sindifuna kudya. Koma anyamata ake, pamodzi ndi mkaziyo anamkakamiza; iye anamvera mau ao. Chomwecho anauka pansi, nakhala pakama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakana ndipo anati, “Ayi, ine sindidya.” Koma nduna zake pamodzi ndi mkaziyo anamuwumiriza, ndipo anawamvera. Choncho anadzuka pansi nakhala pa bedi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye anakana, nati, Sindifuna kudya. Koma anyamata ace, pamodzi ndi mkaziyo anamkangamiza; iyenamvera mau ao. Comweco anauka pansi, nakhala pakama.