1 Samuel 28:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adadzapereka bulediyo kwa Saulo ndi nduna zake, ndipo onse adadya. Pambuyo pake adanyamuka, nachokapo usiku womwewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nabwera nazo kwa Saulo ndi kwa anyamata ake; nadya iwowa. Atatero ananyamuka, nachoka usiku womwewo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anapereka bulediyo kwa Sauli ndi nduna zake ndipo anadya. Pambuyo pake ananyamuka kupita kwawo usiku womwewo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nabwera nazo kwa Sauli ndi kwa anyamata ace; nadya iwowa. Atatero ananyamuka, nacoka usiku womwewo.